Ekisodo 22:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Musachitire nkhanza mlendo wokhala pakati panu kapena kum’pondereza,+ chifukwa anthu inu munalinso alendo m’dziko la Iguputo.+ Deuteronomo 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iye amaperekera chiweruzo ana amasiye* ndi akazi amasiye,+ ndipo amakonda mlendo wokhala pakati panu+ moti amam’patsa mkate ndi chofunda.
21 “Musachitire nkhanza mlendo wokhala pakati panu kapena kum’pondereza,+ chifukwa anthu inu munalinso alendo m’dziko la Iguputo.+
18 Iye amaperekera chiweruzo ana amasiye* ndi akazi amasiye,+ ndipo amakonda mlendo wokhala pakati panu+ moti amam’patsa mkate ndi chofunda.