Deuteronomo 28:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova adzakuchititsa kukhala kumutu osati kumchira. Pamenepo udzangokhala pamwamba+ ndipo sudzakhala m’munsi, chifukwa ukumvera malamulo+ a Yehova Mulungu wako amene ndikukupatsa lero kuti uwasunge ndi kuwatsatira. 1 Mafumu 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iye ankalamulira chilichonse kumbali yakuno ya Mtsinje,+ kuchokera ku Tifisa mpaka ku Gaza.+ Ankalamulira mafumu onse a mbali yakuno ya Mtsinje,+ ndipo m’zigawo zake zonse munali mtendere.+
13 Yehova adzakuchititsa kukhala kumutu osati kumchira. Pamenepo udzangokhala pamwamba+ ndipo sudzakhala m’munsi, chifukwa ukumvera malamulo+ a Yehova Mulungu wako amene ndikukupatsa lero kuti uwasunge ndi kuwatsatira.
24 Iye ankalamulira chilichonse kumbali yakuno ya Mtsinje,+ kuchokera ku Tifisa mpaka ku Gaza.+ Ankalamulira mafumu onse a mbali yakuno ya Mtsinje,+ ndipo m’zigawo zake zonse munali mtendere.+