2 Mafumu 23:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma m’chaka cha 18 cha Mfumu Yosiya, iwo anachitira Yehova pasika ameneyu ku Yerusalemu.+ Yohane 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano pasika+ wa Ayuda anali pafupi. Choncho Yesu ananyamuka kupita ku Yerusalemu.+ Yohane 11:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Tsopano pasika+ wa Ayuda anali pafupi, ndipo anthu ochuluka anachoka m’midzi ndi kupita ku Yerusalemu pasikayo asanafike, kuti akachite mwambo wa kudziyeretsa.+
55 Tsopano pasika+ wa Ayuda anali pafupi, ndipo anthu ochuluka anachoka m’midzi ndi kupita ku Yerusalemu pasikayo asanafike, kuti akachite mwambo wa kudziyeretsa.+