Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 23:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 “Zipatso zoyamba kucha zabwino koposa zam’munda mwanu muzibwera nazo kunyumba ya Yehova Mulungu wanu.+

      “Musawiritse mwana wa mbuzi mumkaka wa mayi wake.+

  • Numeri 18:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Ndakupatsa iwe zipatso zoyambirira+ za mafuta onse abwino koposa, vinyo yense watsopano wabwino koposa, ndi mbewu zabwino koposa, zimene anthu azizipereka kwa Yehova.+

  • Deuteronomo 26:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Choncho ndabweretsa zipatso zoyambirira mwa zipatso za m’dziko limene Yehova anandipatsa.’+

      “Pamenepo uzikaziika pamaso pa Yehova Mulungu wako ndi kugwada pamaso pa Yehova Mulungu wako.+

  • 2 Mbiri 31:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Kuwonjezera pamenepo, Hezekiya anauza anthu okhala mu Yerusalemu kuti apereke gawo loyenera kupita kwa ansembe+ ndi Alevi,+ n’cholinga choti iwo azitsatira+ mosamala chilamulo cha Yehova.+

  • Nehemiya 12:44
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 Kuwonjezera apo, pa tsiku limenelo anaika amuna kuti aziyang’anira zipinda+ zosungiramo zinthu zosiyanasiyana,+ zopereka,+ mbewu zoyambirira+ ndi chakhumi.+ Anawapatsa udindo wosonkhanitsira m’zipindamo gawo loyenera kuperekedwa kwa ansembe ndi Alevi+ malinga ndi chilamulo,+ kuchokera m’minda yonse ya m’mizinda yawo. Yuda anali kusangalala chifukwa ansembe ndi Alevi+ anali kuchita utumiki wawo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena