Numeri 21:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsopano Aisiraeli anatuma amithenga kupita kwa Sihoni+ mfumu ya Aamori kukanena kuti: Numeri 21:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma Aisiraeli anapha anthuwo ndi lupanga+ n’kuwalanda dziko lawo,+ kuyambira kuchigwa cha Arinoni+ mpaka kuchigwa cha Yaboki,+ pafupi ndi ana a Amoni, chifukwa Yazeri+ ali kumalire kwa ana a Amoni.+
24 Koma Aisiraeli anapha anthuwo ndi lupanga+ n’kuwalanda dziko lawo,+ kuyambira kuchigwa cha Arinoni+ mpaka kuchigwa cha Yaboki,+ pafupi ndi ana a Amoni, chifukwa Yazeri+ ali kumalire kwa ana a Amoni.+