Numeri 34:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “‘Chigawo chanu chakum’mwera chiyenera kuyambira kuchipululu cha Zini, kumalire a Edomu.+ Malire anu a kum’mwera ayenera kuchokera kumathero a Nyanja Yamchere,+ kum’mawa. Deuteronomo 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Musalimbane nawo, chifukwa sindikupatsani dziko lawo, ngakhale kachigawo kokwana phazi limodzi lokha. Ndinapereka phiri la Seiri kwa Esau kuti likhale malo ake.+
3 “‘Chigawo chanu chakum’mwera chiyenera kuyambira kuchipululu cha Zini, kumalire a Edomu.+ Malire anu a kum’mwera ayenera kuchokera kumathero a Nyanja Yamchere,+ kum’mawa.
5 Musalimbane nawo, chifukwa sindikupatsani dziko lawo, ngakhale kachigawo kokwana phazi limodzi lokha. Ndinapereka phiri la Seiri kwa Esau kuti likhale malo ake.+