-
1 Samueli 17:52Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
52 Zitatero, amuna a Isiraeli ndi Yuda anayamba kufuula ndi kuthamangitsa+ Afilisiti kukafika kuchigwa,+ mpaka kuzipata za mzinda wa Ekironi.+ Afilisiti amene anavulazidwa mosachiritsika anali kugwa m’njira yochokera ku Saaraimu,+ moti mitembo yawo inali paliponse mpaka kumizinda ya Gati ndi Ekironi.
-