Genesis 48:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano ana awiri amene unabereka ku Iguputo kuno ine ndisanabwere, ndi ana anga.+ Efuraimu ndi Manase akhala ana anga monga alili Rubeni ndi Simiyoni.+ Yoswa 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ana a Yosefe analankhula ndi Yoswa kuti: “N’chifukwa chiyani mwatipatsa gawo limodzi lokha+ kuti likhale cholowa chathu, chikhalirecho tilipo anthu ochuluka popeza Yehova watidalitsa mpaka pano?”+
5 Tsopano ana awiri amene unabereka ku Iguputo kuno ine ndisanabwere, ndi ana anga.+ Efuraimu ndi Manase akhala ana anga monga alili Rubeni ndi Simiyoni.+
14 Ana a Yosefe analankhula ndi Yoswa kuti: “N’chifukwa chiyani mwatipatsa gawo limodzi lokha+ kuti likhale cholowa chathu, chikhalirecho tilipo anthu ochuluka popeza Yehova watidalitsa mpaka pano?”+