Genesis 50:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yosefe anakhalabe ndi moyo mpaka kuona ana a Efuraimu a m’badwo wachitatu.+ Anaonanso ana a Makiri+ mwana wa Manase. Onsewo anabadwira pamiyendo pa Yosefe.+ Numeri 32:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Choncho Mose anapereka mzinda wa Giliyadi kwa Makiri mwana wa Manase, ndipo iye anayamba kukhala mmenemo.+
23 Yosefe anakhalabe ndi moyo mpaka kuona ana a Efuraimu a m’badwo wachitatu.+ Anaonanso ana a Makiri+ mwana wa Manase. Onsewo anabadwira pamiyendo pa Yosefe.+
40 Choncho Mose anapereka mzinda wa Giliyadi kwa Makiri mwana wa Manase, ndipo iye anayamba kukhala mmenemo.+