1 Samueli 31:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamapeto pake, anakaika zida zakezo+ m’nyumba ya zifaniziro za Asitoreti,+ ndipo anapachika mtembo wake pakhoma mumzinda wa Beti-sani.+ 1 Mafumu 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Baana mwana wa Ahiludi, ku Taanaki+ ndi ku Megido+ ndi ku Beti-seani+ konse, pafupi ndi Zeretani+ kumunsi kwa Yezereeli,+ kuchokera ku Beti-seani kukafika ku Abele-mehola+ mpaka kuchigawo cha Yokimeamu,+
10 Pamapeto pake, anakaika zida zakezo+ m’nyumba ya zifaniziro za Asitoreti,+ ndipo anapachika mtembo wake pakhoma mumzinda wa Beti-sani.+
12 Baana mwana wa Ahiludi, ku Taanaki+ ndi ku Megido+ ndi ku Beti-seani+ konse, pafupi ndi Zeretani+ kumunsi kwa Yezereeli,+ kuchokera ku Beti-seani kukafika ku Abele-mehola+ mpaka kuchigawo cha Yokimeamu,+