Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 17:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Mizinda yotsatirayi ya m’gawo la Isakara ndi Aseri, pamodzi ndi anthu ake ndi midzi yake yozungulira, inali ya Manase:+ Beti-seani,+ Ibuleamu,+ Dori,+ Eni-dori,+ Taanaki,+ ndi Megido.+ Madera atatu amapiri analinso ake.

  • Oweruza 1:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Manase+ sanatenge mzinda wa Beti-seani+ ndi midzi yake yozungulira, Taanaki+ ndi midzi yake yozungulira, ndipo sanapitikitse anthu okhala mumzinda wa Dori+ ndi midzi yake yozungulira, anthu a mumzinda wa Ibuleamu+ ndi midzi yake yozungulira, ndi anthu okhala mumzinda wa Megido+ ndi midzi yake yozungulira. Akananiwo anakakamirabe kukhala m’dziko limeneli.+

  • 2 Samueli 21:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Chotero Davide anapita kukatenga mafupa a Sauli+ ndi mafupa a Yonatani mwana wake kwa anthu a ku Yabesi-giliyadi.+ Anthuwo ndiwo anaba mitembo ya Sauli ndi Yonatani m’bwalo la mzinda wa Beti-sani,+ kumene Afilisiti anali ataipachika,+ tsiku limene anapha Sauli paphiri la Giliboa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena