Yoswa 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Fuko la Manase, mwana woyamba wa Yosefe,+ linapatsidwa gawo lake.+ Makiri+ mwana woyamba wa Manase,+ bambo wake wa Giliyadi,+ anali mwamuna wamphamvu pankhondo,+ ndipo gawo lake linali Giliyadi+ ndi Basana.
17 Fuko la Manase, mwana woyamba wa Yosefe,+ linapatsidwa gawo lake.+ Makiri+ mwana woyamba wa Manase,+ bambo wake wa Giliyadi,+ anali mwamuna wamphamvu pankhondo,+ ndipo gawo lake linali Giliyadi+ ndi Basana.