Numeri 26:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ana aamuna a Manase+ anali Makiri+ amene anali kholo la banja la Amakiri. Makiri anabereka Giliyadi.+ Giliyadi anali kholo la banja la Agiliyadi. 1 Mbiri 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kenako Gesuri+ ndi Siriya+ analanda Havoti-yairi.+ Analandanso Kenati+ ndi midzi yake yozungulira, mizinda 60. Onsewa anali ana a Makiri, bambo wa Giliyadi. 1 Mbiri 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mwana wa Manase+ yemwe mdzakazi wake wachisiriya anam’berekera, anali Asiriyeli. (Mdzakaziyo anabereka Makiri,+ bambo wa Giliyadi.
29 Ana aamuna a Manase+ anali Makiri+ amene anali kholo la banja la Amakiri. Makiri anabereka Giliyadi.+ Giliyadi anali kholo la banja la Agiliyadi.
23 Kenako Gesuri+ ndi Siriya+ analanda Havoti-yairi.+ Analandanso Kenati+ ndi midzi yake yozungulira, mizinda 60. Onsewa anali ana a Makiri, bambo wa Giliyadi.
14 Mwana wa Manase+ yemwe mdzakazi wake wachisiriya anam’berekera, anali Asiriyeli. (Mdzakaziyo anabereka Makiri,+ bambo wa Giliyadi.