Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 50:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Yosefe anakhalabe ndi moyo mpaka kuona ana a Efuraimu a m’badwo wachitatu.+ Anaonanso ana a Makiri+ mwana wa Manase. Onsewo anabadwira pamiyendo pa Yosefe.+

  • Numeri 26:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Ana aamuna a Manase+ anali Makiri+ amene anali kholo la banja la Amakiri. Makiri anabereka Giliyadi.+ Giliyadi anali kholo la banja la Agiliyadi.

  • Numeri 27:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Kenako ana aakazi a Tselofekadi+ anafika kwa Mose. Tselofekadi anali mwana wa Heferi, Heferi anali mwana wa Giliyadi, Giliyadi anali mwana wa Makiri, ndipo Makiri anali mwana wa Manase.+ Onsewa anali ochokera kumabanja a Manase mwana wa Yosefe. Ana aakazi a Tselofekadi amenewo mayina awo anali Mala, Nowa, Hogila, Milika ndi Tiriza.+

  • Deuteronomo 3:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Makiri+ ndinam’patsa Giliyadi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena