Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 41:51
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 51 Mwana woyambayo Yosefe anamutcha dzina lakuti Manase,*+ chifukwa anati, “Mulungu wandiiwalitsa mavuto anga onse, ndi nyumba yonse ya bambo anga.”+

  • Genesis 48:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Yosefe anauza bambo ake kuti: “Ayi bambo, musatero ayi. Mwana woyamba ndi uyu.+ Ikani dzanja lanu lamanja pamutu pake.”

  • Deuteronomo 21:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pakuti ayenera kuvomereza kuti mwana wamwamuna wa mkazi wake wosakondedwayo ndiye woyamba kubadwa. Azivomereza mwa kum’patsa magawo awiri pa chilichonse chimene ali nacho,+ chifukwa mwanayo ndiye chiyambi cha mphamvu zake zobereka.+ Mwana ameneyo ndiye woyenera kulandira udindo wa mwana woyamba kubadwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena