Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 28:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndiyeno Afilisiti anasonkhana pamodzi ndi kupita kukamanga msasa ku Sunemu.+ Nayenso Sauli anasonkhanitsa Aisiraeli onse pamodzi ndi kumanga msasa ku Giliboa.+

  • 1 Samueli 31:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Tsopano Afilisiti anali kumenyana ndi Isiraeli,+ ndipo amuna a Isiraeli anathawa pamaso pa Afilisiti, moti anali kuphedwa+ m’phiri la Giliboa.+

  • 2 Samueli 1:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Mnyamatayo anayankha kuti: “Ndinapezeka kuti ndili paphiri la Giliboa,+ ndipo ndinaona Sauli atatsamira mkondo+ wake. Zili choncho, ndinaona asilikali oyenda m’magaleta ndi asilikali okwera pamahatchi* akumuyandikira.+

  • 2 Samueli 1:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Inu mapiri a Giliboa,+ musalole kuti mame kapena mvula igwe pa inu. Musalole kuti minda imene ili pa inu ibale zipatso zokaperekedwa kwa Mulungu.*+

      Chifukwa pa inu chishango cha amuna amphamvu chinadetsedwa,

      Chishango cha Sauli, moti palibenso chishango chimene chinadzozedwa ndi mafuta.+

  • 1 Mbiri 10:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ndiyeno tsiku lotsatira, Afilisiti atabwera kudzavula zovala+ anthu ophedwa, anapeza Sauli ndi ana ake atafa paphiri la Giliboa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena