Yoswa 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Aefuraimu analephera kupitikitsa Akanani+ amene anali kukhala ku Gezeri.+ Choncho Akananiwo akukhalabe pakati pa Aefuraimu mpaka lero,+ ndipo anayamba kuwagwiritsa ntchito yaukapolo.+ Yoswa 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ana a Manase analephera kulanda mizindayi,+ moti Akanani anakakamira kukhalabe m’derali.+ Oweruza 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yehova anakhalabe ndi fuko la Yuda, moti linalanda dera lamapiri, koma silinathe kupitikitsa anthu okhala m’chigwa, chifukwa chakuti anthuwo anali ndi magaleta*+ okhala ndi zitsulo zazitali zakuthwa za m’mawilo.+
10 Aefuraimu analephera kupitikitsa Akanani+ amene anali kukhala ku Gezeri.+ Choncho Akananiwo akukhalabe pakati pa Aefuraimu mpaka lero,+ ndipo anayamba kuwagwiritsa ntchito yaukapolo.+
19 Yehova anakhalabe ndi fuko la Yuda, moti linalanda dera lamapiri, koma silinathe kupitikitsa anthu okhala m’chigwa, chifukwa chakuti anthuwo anali ndi magaleta*+ okhala ndi zitsulo zazitali zakuthwa za m’mawilo.+