Deuteronomo 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Arefai+ anali kuonedwanso ngati Aanaki,+ ndipo Amowabu anali kutcha Arefaiwo kuti Aemi. 2 Samueli 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Afilisitiwo anafika ndi kuyamba kuyendayenda m’chigwa cha Arefai.+ Yesaya 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Munthu wokolola akamadzadula tirigu m’munda ndipo dzanja lake likamadzakolola ngala za tirigu,+ adzakhala ngati munthu wokunkha ngala za tirigu m’chigwa cha Arefai.+
5 Munthu wokolola akamadzadula tirigu m’munda ndipo dzanja lake likamadzakolola ngala za tirigu,+ adzakhala ngati munthu wokunkha ngala za tirigu m’chigwa cha Arefai.+