8 “Mlandu wofuna chigamulo ukakukulira kwambiri,+ monga mlandu wokhudza kukhetsa magazi,+ mlandu umene munthu wakasuma,+ mlandu wokhudza zachiwawa kapena mkangano+ umene wachitika mumzinda wanu, pamenepo uzinyamuka ndi kupita kumalo amene Yehova Mulungu wako adzasankhe.+