Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 19:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Zitatero, aliyense amene anaona zimenezo anati: “Zoterezi sizinachitikepo kapena kuonekapo kuchokera pa tsiku limene ana a Isiraeli anatuluka m’dziko la Iguputo mpaka lero. Iganizireni mofatsa nkhaniyi, munenepo maganizo+ anu ndipo tigwirizane.”

  • Miyambo 11:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pakakhala popanda malangizo anzeru, anthu amagwa.+ Koma pakakhala aphungu ochuluka anthu amapulumuka.+

  • Miyambo 13:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Chifukwa cha kudzikuza, munthu amangoyambitsa mavuto,+ koma anthu amene amakhala pamodzi n’kumakambirana amakhala ndi nzeru.+

  • Miyambo 20:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Zolinga zimakhazikika anthu akakambirana,+ ndipo uzitsatira malangizo anzeru pomenya nkhondo yako.+

  • Miyambo 24:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Iweyo udzatha kumenya nkhondo yako potsatira malangizo anzeru,+ ndipo pakakhala aphungu ochuluka anthu amapulumuka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena