Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 6:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndipo Eleazara mwana wa Aroni,+ anatenga mwana wamkazi wa Putieli kukhala mkazi wake. Ndipo iye anam’berekera Pinihasi.+

      Amenewa ndiwo atsogoleri a mabanja a m’fuko la Levi, malinga ndi mzere wobadwira wa makolo awo.+

  • Numeri 25:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Koma Pinihasi+ mwana wa Eleazara, mdzukulu wa wansembe Aroni, ataona zimenezi nthawi yomweyo ananyamuka pakati pa khamulo n’kutenga mkondo waung’ono m’dzanja lake.

  • Yoswa 22:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kenako ana a Isiraeli anatumiza+ Pinihasi+ mwana wa wansembe Eleazara, kwa ana a Rubeni, ana a Gadi, ndi hafu ya fuko la Manase, ku Giliyadi.

  • Yoswa 24:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Nayenso Eleazara mwana wa Aroni anamwalira.+ Choncho anamuika m’manda m’phiri la Pinihasi mwana wake,+ limene anapatsidwa m’dera lamapiri la Efuraimu.

  • Salimo 106:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Pinihasi ataimirira ndi kuchitapo kanthu,+

      Mliriwo unatha.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena