Oweruza 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye anadzakhala ndi ana 30 aamuna amene anali kuyenda pa abulu 30,+ ndipo iwo anali ndi mizinda 30. Mizinda imeneyi ikutchedwabe kuti Havoti-yairi*+ kufikira lero, ndipo ili m’dziko la Giliyadi. Oweruza 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye anabereka ana aamuna 40 ndipo anali ndi zidzukulu 30. Onsewa anali kuyenda pa abulu 70.+ Ndipo Abidoni anaweruza Isiraeli zaka 8.
4 Iye anadzakhala ndi ana 30 aamuna amene anali kuyenda pa abulu 30,+ ndipo iwo anali ndi mizinda 30. Mizinda imeneyi ikutchedwabe kuti Havoti-yairi*+ kufikira lero, ndipo ili m’dziko la Giliyadi.
14 Iye anabereka ana aamuna 40 ndipo anali ndi zidzukulu 30. Onsewa anali kuyenda pa abulu 70.+ Ndipo Abidoni anaweruza Isiraeli zaka 8.