Oweruza 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inu okwera abulu ofiirira,+Inu okhala pansalu zokwera mtengo,Ndi inu oyenda mumsewu,Ganizirani ntchito za Mulungu izi:+ Oweruza 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye anabereka ana aamuna 40 ndipo anali ndi zidzukulu 30. Onsewa anali kuyenda pa abulu 70.+ Ndipo Abidoni anaweruza Isiraeli zaka 8.
10 Inu okwera abulu ofiirira,+Inu okhala pansalu zokwera mtengo,Ndi inu oyenda mumsewu,Ganizirani ntchito za Mulungu izi:+
14 Iye anabereka ana aamuna 40 ndipo anali ndi zidzukulu 30. Onsewa anali kuyenda pa abulu 70.+ Ndipo Abidoni anaweruza Isiraeli zaka 8.