Oweruza 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inu okwera abulu ofiirira,+Inu okhala pansalu zokwera mtengo,Ndi inu oyenda mumsewu,Ganizirani ntchito za Mulungu izi:+ Oweruza 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye anadzakhala ndi ana 30 aamuna amene anali kuyenda pa abulu 30,+ ndipo iwo anali ndi mizinda 30. Mizinda imeneyi ikutchedwabe kuti Havoti-yairi*+ kufikira lero, ndipo ili m’dziko la Giliyadi.
10 Inu okwera abulu ofiirira,+Inu okhala pansalu zokwera mtengo,Ndi inu oyenda mumsewu,Ganizirani ntchito za Mulungu izi:+
4 Iye anadzakhala ndi ana 30 aamuna amene anali kuyenda pa abulu 30,+ ndipo iwo anali ndi mizinda 30. Mizinda imeneyi ikutchedwabe kuti Havoti-yairi*+ kufikira lero, ndipo ili m’dziko la Giliyadi.