Salimo 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ena akunena za magaleta* ndipo ena akunena za mahatchi,*+Koma ife tidzanena za dzina la Yehova Mulungu wathu.+ Salimo 147:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iye sadalira mphamvu za hatchi,+Kapena liwiro la miyendo ya munthu.+ Miyambo 21:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Hatchi* anaikonzera tsiku la nkhondo,+ koma Yehova ndiye amapulumutsa.+ Yesaya 5:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mivi yawo ndi yakuthwa ndipo mauta awo onse ndi okungika.+ Ziboda za mahatchi awo n’zolimba ngati mwala wa nsangalabwi.+ Mawilo a magaleta awo ali ngati mphepo yamkuntho.+
7 Ena akunena za magaleta* ndipo ena akunena za mahatchi,*+Koma ife tidzanena za dzina la Yehova Mulungu wathu.+
28 Mivi yawo ndi yakuthwa ndipo mauta awo onse ndi okungika.+ Ziboda za mahatchi awo n’zolimba ngati mwala wa nsangalabwi.+ Mawilo a magaleta awo ali ngati mphepo yamkuntho.+