Levitiko 27:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Munthu aliyense woperekedwa kwa Mulungu kuti awonongedwe sangathe kuwomboledwa.+ Ameneyo aziphedwa ndithu.+ Deuteronomo 20:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mizinda yokhayi ya anthu awa a mitundu ina imene Yehova Mulungu wanu akukupatsani monga cholowa, ndi imene simuyenera kusiyamo chilichonse chopuma chili chamoyo,+ Yoswa 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Aliyense amene anali mumzindawo anamupha ndi lupanga, kuyambira amuna, akazi, anyamata ndi nkhalamba zomwe. Anaphanso ng’ombe, nkhosa, ndi abulu.+
29 Munthu aliyense woperekedwa kwa Mulungu kuti awonongedwe sangathe kuwomboledwa.+ Ameneyo aziphedwa ndithu.+
16 Mizinda yokhayi ya anthu awa a mitundu ina imene Yehova Mulungu wanu akukupatsani monga cholowa, ndi imene simuyenera kusiyamo chilichonse chopuma chili chamoyo,+
21 Aliyense amene anali mumzindawo anamupha ndi lupanga, kuyambira amuna, akazi, anyamata ndi nkhalamba zomwe. Anaphanso ng’ombe, nkhosa, ndi abulu.+