Yoswa 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ansembe 7 aziyenda patsogolo pa Likasa atanyamula malipenga 7 a nyanga za nkhosa zamphongo. Pa tsiku la 7 mudzagube kuzungulira mzindawo maulendo 7, ansembewo akuliza malipenga.+ Oweruza 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ine ndikaliza lipenga la nyanga ya nkhosa pamodzi ndi anthu onse a m’gulu langa, nanunso mulize malipenga anu kuzungulira msasa wonse,+ ndipo munene kuti, ‘Nkhondo ya Yehova+ ndi ya Gidiyoni!’”
4 Ansembe 7 aziyenda patsogolo pa Likasa atanyamula malipenga 7 a nyanga za nkhosa zamphongo. Pa tsiku la 7 mudzagube kuzungulira mzindawo maulendo 7, ansembewo akuliza malipenga.+
18 Ine ndikaliza lipenga la nyanga ya nkhosa pamodzi ndi anthu onse a m’gulu langa, nanunso mulize malipenga anu kuzungulira msasa wonse,+ ndipo munene kuti, ‘Nkhondo ya Yehova+ ndi ya Gidiyoni!’”