1 Samueli 17:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Ndipo mpingo wonsewu udziwa kuti Yehova sapulumutsa ndi lupanga kapena mkondo,+ chifukwa Yehova ndiye mwini nkhondo,+ moti apereka anthu inu m’manja mwathu.”+ 2 Mbiri 20:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ulendo uno simufunikira kumenya nkhondo.+ Khalani m’malo anu, imani chilili+ ndi kuona Yehova akukupulumutsani.+ Inu Ayuda ndi anthu a ku Yerusalemu, musaope kapena kuchita mantha.+ Mawa mupite kukakumana nawo ndipo Yehova akhala nanu.’”+
47 Ndipo mpingo wonsewu udziwa kuti Yehova sapulumutsa ndi lupanga kapena mkondo,+ chifukwa Yehova ndiye mwini nkhondo,+ moti apereka anthu inu m’manja mwathu.”+
17 Ulendo uno simufunikira kumenya nkhondo.+ Khalani m’malo anu, imani chilili+ ndi kuona Yehova akukupulumutsani.+ Inu Ayuda ndi anthu a ku Yerusalemu, musaope kapena kuchita mantha.+ Mawa mupite kukakumana nawo ndipo Yehova akhala nanu.’”+