Ekisodo 23:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Utalikirane ndi mawu onama.+ Usaphe munthu wosalakwa ndi munthu wolungama, chifukwa woipa sindidzamuyesa wolungama.+ Oweruza 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho abale a mayi ake anayamba kulankhula mawu onsewa nzika zonse za Sekemu zikumva, moti mitima yawo inakonda Abimeleki,+ chifukwa anati: “Ndi m’bale wathu ameneyu.”+
7 “Utalikirane ndi mawu onama.+ Usaphe munthu wosalakwa ndi munthu wolungama, chifukwa woipa sindidzamuyesa wolungama.+
3 Choncho abale a mayi ake anayamba kulankhula mawu onsewa nzika zonse za Sekemu zikumva, moti mitima yawo inakonda Abimeleki,+ chifukwa anati: “Ndi m’bale wathu ameneyu.”+