Genesis 30:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno Leya anati: “Mulungu wandipatsadi mphoto yabwino. Tsopano mwamuna wanga ayamba kukondwera nane,+ chifukwa ndam’berekera ana aamuna 6.”+ Chotero Leya anatcha mwanayo dzina lakuti Zebuloni.*+ Yoswa 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Maere achitatu+ anagwera ana a Zebuloni+ potsata mabanja awo. Malire a cholowa chawo anayambira ku Saridi Oweruza 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Amene anali m’chigwa anachokera m’fuko la Efuraimu,+Ndipo iwo anali ndi iwe Benjamini, pakati pa anthu a mtundu wako.Atsogoleri a asilikali anachokera kwa Makiri,+Ndipo osunga zida za mlembi, anachokera m’fuko la Zebuloni.+
20 Ndiyeno Leya anati: “Mulungu wandipatsadi mphoto yabwino. Tsopano mwamuna wanga ayamba kukondwera nane,+ chifukwa ndam’berekera ana aamuna 6.”+ Chotero Leya anatcha mwanayo dzina lakuti Zebuloni.*+
10 Maere achitatu+ anagwera ana a Zebuloni+ potsata mabanja awo. Malire a cholowa chawo anayambira ku Saridi
14 Amene anali m’chigwa anachokera m’fuko la Efuraimu,+Ndipo iwo anali ndi iwe Benjamini, pakati pa anthu a mtundu wako.Atsogoleri a asilikali anachokera kwa Makiri,+Ndipo osunga zida za mlembi, anachokera m’fuko la Zebuloni.+