Oweruza 13:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kenako mzimu wa Yehova+ unayamba kugwira ntchito pa iye ku Mahane-dani+ pakati pa Zora+ ndi Esitaoli.+ Oweruza 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno mzimu wa Yehova unayamba kugwira ntchito pa iye,+ moti anakhadzula mkangowo pakati ngati mmene munthu angakhadzulire kamwana ka mbuzi. Iye analibe chida chilichonse m’manja mwake. Zimene anachitazi sanauze bambo kapena mayi ake. Zekariya 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho iye anandiuza kuti: “Yehova wauza Zerubabele kuti, ‘“Kuti zinthu zonsezi zichitike, sipakufunika gulu lankhondo,+ kapena mphamvu,+ koma mzimu wanga,”+ watero Yehova wa makamu.
25 Kenako mzimu wa Yehova+ unayamba kugwira ntchito pa iye ku Mahane-dani+ pakati pa Zora+ ndi Esitaoli.+
6 Ndiyeno mzimu wa Yehova unayamba kugwira ntchito pa iye,+ moti anakhadzula mkangowo pakati ngati mmene munthu angakhadzulire kamwana ka mbuzi. Iye analibe chida chilichonse m’manja mwake. Zimene anachitazi sanauze bambo kapena mayi ake.
6 Choncho iye anandiuza kuti: “Yehova wauza Zerubabele kuti, ‘“Kuti zinthu zonsezi zichitike, sipakufunika gulu lankhondo,+ kapena mphamvu,+ koma mzimu wanga,”+ watero Yehova wa makamu.