4 Malirewo akadutse kum’mwera kwa chitunda cha Akirabimu+ kulowera ku Zini, n’kuloweranso kum’mwera kwa Kadesi-barinea.+ Kenako akakhotere ku Hazara-adara+ n’kukafika ku Azimoni.
3 Malirewo analowera kum’mwera kuchitunda cha Akirabimu+ n’kukafika ku Zini.+ Kenako anakwera kuchokera kum’mwera kupita ku Kadesi-barinea,+ n’kukadutsa ku Hezironi mpaka ku Adara, n’kuzungulira kukafika ku Karika.