Oweruza 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma mkaziyo anapitiriza kulira pamaso pa Samisoni kwa masiku 7 a phwandolo. Pamapeto pake, pa tsiku la 7, Samisoni anauza mkaziyo tanthauzo lake chifukwa anamuumiriza.+ Kenako mkaziyo anaulula tanthauzo la mwambiwo kwa anthu a mtundu wake.+ Mika 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Musamakhulupirire anzanu. Musamadalire mnzanu wapamtima.+ Samala zonena zako polankhula ndi amene umagona naye pafupi.+
17 Koma mkaziyo anapitiriza kulira pamaso pa Samisoni kwa masiku 7 a phwandolo. Pamapeto pake, pa tsiku la 7, Samisoni anauza mkaziyo tanthauzo lake chifukwa anamuumiriza.+ Kenako mkaziyo anaulula tanthauzo la mwambiwo kwa anthu a mtundu wake.+
5 Musamakhulupirire anzanu. Musamadalire mnzanu wapamtima.+ Samala zonena zako polankhula ndi amene umagona naye pafupi.+