Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 6:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ngakhale abale anga amene, achita zachinyengo+ ngati mtsinje woyenda nthawi yozizira,

      Ngati makwawa a mitsinje yoyenda nthawi yozizira, imene imauma.

  • Salimo 118:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Kuthawira kwa Yehova n’kwabwino+

      Kusiyana ndi kudalira munthu wochokera kufumbi.+

  • Yeremiya 9:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Aliyense wa inu asamale ndi mnzake,+ ndipo musakhulupirire m’bale aliyense.+ Pakuti munthu aliyense amalanda malo a m’bale wake,+ ndipo munthu aliyense amakhala akuyendayenda kunenera mnzake miseche.+

  • Luka 21:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Komanso makolo anu enieniwo,+ abale anu, anthu oyandikana nanu ndi mabwenzi anu, adzakuperekani, ndipo adzapha ena a inu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena