Oweruza 16:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiyeno chifukwa chakuti Delila anapanikiza+ Samisoni ndi mawu ake mosalekeza, ndi kum’chonderera, Samisoni anafika potopa nazo kwambiri.+ Miyambo 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwana wopusa amabweretsa mavuto kwa bambo ake,+ ndipo mkazi wolongolola ali ngati denga* lodontha limene limathawitsa munthu.+ Miyambo 21:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kuli bwino kukhala m’chipululu kusiyana ndi kukhala mokhumudwa ndi mkazi wolongolola.+ Luka 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndithu ndikukuuzani, Adzadzuka ndi kum’patsa zonse zimene akufuna, osati chifukwa chakuti ndi bwenzi lake, koma chifukwa cha kukakamira kwake.+
16 Ndiyeno chifukwa chakuti Delila anapanikiza+ Samisoni ndi mawu ake mosalekeza, ndi kum’chonderera, Samisoni anafika potopa nazo kwambiri.+
13 Mwana wopusa amabweretsa mavuto kwa bambo ake,+ ndipo mkazi wolongolola ali ngati denga* lodontha limene limathawitsa munthu.+
8 Ndithu ndikukuuzani, Adzadzuka ndi kum’patsa zonse zimene akufuna, osati chifukwa chakuti ndi bwenzi lake, koma chifukwa cha kukakamira kwake.+