Miyambo 21:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kuli bwino kukhala m’chipululu kusiyana ndi kukhala mokhumudwa ndi mkazi wolongolola.+ Miyambo 25:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kuli bwino kukhala pakona ya denga la nyumba, kusiyana ndi kukhala m’nyumba limodzi ndi mkazi wolongolola.+ Miyambo 27:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Denga lodontha limene limathawitsa munthu pa tsiku la mvula yosalekeza, limafanana ndi mkazi wolongolola.+ Luka 11:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndithu ndikukuuzani, Adzadzuka ndi kum’patsa zonse zimene akufuna, osati chifukwa chakuti ndi bwenzi lake, koma chifukwa cha kukakamira kwake.+
24 Kuli bwino kukhala pakona ya denga la nyumba, kusiyana ndi kukhala m’nyumba limodzi ndi mkazi wolongolola.+
15 Denga lodontha limene limathawitsa munthu pa tsiku la mvula yosalekeza, limafanana ndi mkazi wolongolola.+
8 Ndithu ndikukuuzani, Adzadzuka ndi kum’patsa zonse zimene akufuna, osati chifukwa chakuti ndi bwenzi lake, koma chifukwa cha kukakamira kwake.+