Yoswa 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yoswa atamva, anawayankha kuti: “Ngati muli ochuluka, kwerani mtunda mupite kunkhalango ya Aperezi+ ndi ya Arefai,+ mukaduleko mitengo n’kutenga deralo, chifukwa dera lamapiri+ la Efuraimu lakucheperani.” Oweruza 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pambuyo pa Abimeleki, panabwera Tola, munthu wa fuko la Isakara, amene anapulumutsa+ Isiraeli. Iye anali kukhala ku Samiri m’dera lamapiri la Efuraimu,+ ndipo anali mwana wa Puwa, amene anali mwana wa Dodo.
15 Yoswa atamva, anawayankha kuti: “Ngati muli ochuluka, kwerani mtunda mupite kunkhalango ya Aperezi+ ndi ya Arefai,+ mukaduleko mitengo n’kutenga deralo, chifukwa dera lamapiri+ la Efuraimu lakucheperani.”
10 Pambuyo pa Abimeleki, panabwera Tola, munthu wa fuko la Isakara, amene anapulumutsa+ Isiraeli. Iye anali kukhala ku Samiri m’dera lamapiri la Efuraimu,+ ndipo anali mwana wa Puwa, amene anali mwana wa Dodo.