Genesis 29:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno iye anawafunsa kuti: “Kodi iye ali bwino?”+ Iwo anayankha kuti: “Ali bwino. Komanso mwana wake Rakele,+ suyo akubwera apoyo ndi nkhosa?”+ Genesis 43:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako Yosefe anawafunsa ngati ali bwino.+ Anawafunsanso kuti: “Kodi bambo anu okalamba amene munkanena aja ali bwino? Kodi adakali ndi moyo?”+
6 Ndiyeno iye anawafunsa kuti: “Kodi iye ali bwino?”+ Iwo anayankha kuti: “Ali bwino. Komanso mwana wake Rakele,+ suyo akubwera apoyo ndi nkhosa?”+
27 Kenako Yosefe anawafunsa ngati ali bwino.+ Anawafunsanso kuti: “Kodi bambo anu okalamba amene munkanena aja ali bwino? Kodi adakali ndi moyo?”+