Genesis 43:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako Yosefe anawafunsa ngati ali bwino.+ Anawafunsanso kuti: “Kodi bambo anu okalamba amene munkanena aja ali bwino? Kodi adakali ndi moyo?”+ 1 Samueli 17:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Nthawi yomweyo, Davide anasiya katundu+ wake m’manja mwa munthu wosamalira katundu,+ ndipo anathamangira kumalo omenyera nkhondo. Atafika kumeneko, anayamba kufunsa za abale ake ngati ali bwino.+
27 Kenako Yosefe anawafunsa ngati ali bwino.+ Anawafunsanso kuti: “Kodi bambo anu okalamba amene munkanena aja ali bwino? Kodi adakali ndi moyo?”+
22 Nthawi yomweyo, Davide anasiya katundu+ wake m’manja mwa munthu wosamalira katundu,+ ndipo anathamangira kumalo omenyera nkhondo. Atafika kumeneko, anayamba kufunsa za abale ake ngati ali bwino.+