1 Samueli 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Motero anafunsiranso+ kwa Yehova, kuti: “Kodi mwamunayu wafika kale pano?” Pamenepo Yehova anayankha kuti: “Uyu wabisala+ pakati pa katunduyu.” 1 Samueli 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako Jese anauza Davide mwana wake kuti: “Tenga tirigu wokazinga+ uyu wokwana muyezo umodzi wa efa ndi mitanda ya mkate 10, upite nazo mofulumira kwa abale ako kumsasa.
22 Motero anafunsiranso+ kwa Yehova, kuti: “Kodi mwamunayu wafika kale pano?” Pamenepo Yehova anayankha kuti: “Uyu wabisala+ pakati pa katunduyu.”
17 Kenako Jese anauza Davide mwana wake kuti: “Tenga tirigu wokazinga+ uyu wokwana muyezo umodzi wa efa ndi mitanda ya mkate 10, upite nazo mofulumira kwa abale ako kumsasa.