Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 1:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 1 Ndiyeno zinachitika kuti Yoswa atamwalira,+ ana a Isiraeli anafunsira+ kwa Yehova kuti: “Ndani wa ife adzayamba kupita kwa Akanani kukamenyana nawo?”

  • Oweruza 20:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ndipo ana a Isiraeli ananyamuka ndi kupita ku Beteli kukafunsira kwa Mulungu,+ kuti: “Ndani wa ife ayenera kutitsogolera kunkhondo yomenyana ndi ana a Benjamini?”+ Poyankha, Yehova anati: “Yuda akutsogolereni.”+

  • Oweruza 20:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Masiku amenewo Pinihasi,+ mwana wa Eleazara, mwana wa Aroni, ndiye anali kuimirira pafupi ndi likasalo.+ Chotero iye anafunsa kuti: “Kodi ndipitenso kukamenyana ndi ana a m’bale wanga Benjamini kapena ndisapite?”+ Poyankha, Yehova anati: “Pita, chifukwa mawa ndim’pereka m’dzanja lako.”+

  • 1 Samueli 23:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndiyeno Davide anayamba kufunsira+ kwa Yehova, kuti: “Kodi ndipite kukamenyana ndi Afilisitiwa?” Yehova anayankha Davide kuti: “Pita, ukamenyane ndi Afilisitiwo ndipo ukapulumutse Keila.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena