Rute 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipo pa nthawi ya chakudya Boazi anaitana Rute kuti: “Tabwera kuno udzadye mkate+ ndiponso uziusunsa mu vinyo wowawasayu.” Choncho Rute anadzakhala pansi limodzi ndi okololawo, ndipo Boazi anali kum’patsira mbewu zokazinga,+ iye n’kumadya moti anakhuta mpaka zina kutsala. 1 Samueli 25:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Nthawi yomweyo, Abigayeli+ anafulumira kutenga mitanda 200 ya mkate, mitsuko iwiri ikuluikulu ya vinyo,+ anapha nkhosa zisanu,+ anatenganso miyezo ya seya* isanu ya tirigu wokazinga,+ mphesa zouma zoumba pamodzi 100+ ndi nkhuyu zouma zoumba pamodzi 200+ ndi kuzikweza pa abulu. 2 Samueli 17:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 anabweretsa makama, mabeseni, ziwiya zadothi, tirigu, balere, ufa,+ tirigu wokazinga,+ nyemba zikuluzikulu,+ mphodza+ ndi tirigu wowamba.
14 Ndipo pa nthawi ya chakudya Boazi anaitana Rute kuti: “Tabwera kuno udzadye mkate+ ndiponso uziusunsa mu vinyo wowawasayu.” Choncho Rute anadzakhala pansi limodzi ndi okololawo, ndipo Boazi anali kum’patsira mbewu zokazinga,+ iye n’kumadya moti anakhuta mpaka zina kutsala.
18 Nthawi yomweyo, Abigayeli+ anafulumira kutenga mitanda 200 ya mkate, mitsuko iwiri ikuluikulu ya vinyo,+ anapha nkhosa zisanu,+ anatenganso miyezo ya seya* isanu ya tirigu wokazinga,+ mphesa zouma zoumba pamodzi 100+ ndi nkhuyu zouma zoumba pamodzi 200+ ndi kuzikweza pa abulu.
28 anabweretsa makama, mabeseni, ziwiya zadothi, tirigu, balere, ufa,+ tirigu wokazinga,+ nyemba zikuluzikulu,+ mphodza+ ndi tirigu wowamba.