2 Samueli 17:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Iwo anabweretsanso uchi,+ mafuta a mkaka,+ wa ng’ombe ndiponso nkhosa. Anabweretsa zinthu zimenezi kuti Davide ndi anthu onse amene anali naye adye.+ Iwo anali kunena kuti: “Anthu amenewa ali ndi njala, atopa ndipo ali ndi ludzu m’chipululu.”+
29 Iwo anabweretsanso uchi,+ mafuta a mkaka,+ wa ng’ombe ndiponso nkhosa. Anabweretsa zinthu zimenezi kuti Davide ndi anthu onse amene anali naye adye.+ Iwo anali kunena kuti: “Anthu amenewa ali ndi njala, atopa ndipo ali ndi ludzu m’chipululu.”+