1 Samueli 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako Jese anauza Davide mwana wake kuti: “Tenga tirigu wokazinga+ uyu wokwana muyezo umodzi wa efa ndi mitanda ya mkate 10, upite nazo mofulumira kwa abale ako kumsasa. 1 Samueli 25:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Nthawi yomweyo, Abigayeli+ anafulumira kutenga mitanda 200 ya mkate, mitsuko iwiri ikuluikulu ya vinyo,+ anapha nkhosa zisanu,+ anatenganso miyezo ya seya* isanu ya tirigu wokazinga,+ mphesa zouma zoumba pamodzi 100+ ndi nkhuyu zouma zoumba pamodzi 200+ ndi kuzikweza pa abulu. 2 Samueli 17:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 anabweretsa makama, mabeseni, ziwiya zadothi, tirigu, balere, ufa,+ tirigu wokazinga,+ nyemba zikuluzikulu,+ mphodza+ ndi tirigu wowamba.
17 Kenako Jese anauza Davide mwana wake kuti: “Tenga tirigu wokazinga+ uyu wokwana muyezo umodzi wa efa ndi mitanda ya mkate 10, upite nazo mofulumira kwa abale ako kumsasa.
18 Nthawi yomweyo, Abigayeli+ anafulumira kutenga mitanda 200 ya mkate, mitsuko iwiri ikuluikulu ya vinyo,+ anapha nkhosa zisanu,+ anatenganso miyezo ya seya* isanu ya tirigu wokazinga,+ mphesa zouma zoumba pamodzi 100+ ndi nkhuyu zouma zoumba pamodzi 200+ ndi kuzikweza pa abulu.
28 anabweretsa makama, mabeseni, ziwiya zadothi, tirigu, balere, ufa,+ tirigu wokazinga,+ nyemba zikuluzikulu,+ mphodza+ ndi tirigu wowamba.