1 Samueli 25:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwamuna ameneyu dzina lake anali Nabala,+ ndipo mkazi wake anali Abigayeli.+ Mkazi wakeyu anali wanzeru kwambiri+ ndi wokongola, koma mwamunayu anali wouma mtima ndi wokonda kuchita zinthu zoipa.+ Mwamuna ameneyu anali wa m’banja la Kalebe.+ 1 Samueli 25:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Abigayeli ataona Davide, nthawi yomweyo anatsika mofulumira pabulu wake. Iye anagwada pamaso pa Davide ndi kuwerama mpaka nkhope yake pansi.+ 1 Samueli 25:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Pamenepo Davide anauza Abigayeli kuti: “Adalitsike Yehova Mulungu wa Isiraeli,+ amene wakutumiza kudzakumana nane lero!
3 Mwamuna ameneyu dzina lake anali Nabala,+ ndipo mkazi wake anali Abigayeli.+ Mkazi wakeyu anali wanzeru kwambiri+ ndi wokongola, koma mwamunayu anali wouma mtima ndi wokonda kuchita zinthu zoipa.+ Mwamuna ameneyu anali wa m’banja la Kalebe.+
23 Abigayeli ataona Davide, nthawi yomweyo anatsika mofulumira pabulu wake. Iye anagwada pamaso pa Davide ndi kuwerama mpaka nkhope yake pansi.+
32 Pamenepo Davide anauza Abigayeli kuti: “Adalitsike Yehova Mulungu wa Isiraeli,+ amene wakutumiza kudzakumana nane lero!