Salimo 41:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Adalitsike Yehova Mulungu wa Isiraeli,+Kuyambira kalekale mpaka kalekale.+Ame! Ame!*+ Salimo 72:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Adalitsike Yehova Mulungu, Mulungu wa Isiraeli,+Iye yekha amene akuchita ntchito zodabwitsa.+