Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Rute 4:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Obedi anabereka Jese,+ ndipo Jese anabereka Davide.+

  • 1 Samueli 20:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Tsiku lotsatizana ndi tsiku lokhala mwezi, tsiku lachiwiri, mpando wa Davide unakhalabe wopanda munthu. Choncho Sauli anafunsa mwana wake Yonatani kuti: “N’chifukwa chiyani mwana wa Jese+ sanabwere ku chakudya dzulo ndi lero?”

  • 1 Samueli 25:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pamenepo Nabala anayankha atumiki a Davide kuti: “Kodi Davide ndani,+ ndipo mwana wa Jese ndani? Masiku ano atumiki amene akuthawa ambuye awo achuluka kwabasi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena