Miyambo 28:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mtsogoleri amene ali wosazindikira kwenikweni amakhalanso wakatangale kwambiri,+ koma munthu wodana ndi phindu lachinyengo+ adzachulukitsa masiku ake. Mlaliki 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwana wosauka koma wanzeru ali bwino+ kuposa mfumu yokalamba koma yopusa,+ imene sionanso kufunika kochenjezedwa.+
16 Mtsogoleri amene ali wosazindikira kwenikweni amakhalanso wakatangale kwambiri,+ koma munthu wodana ndi phindu lachinyengo+ adzachulukitsa masiku ake.
13 Mwana wosauka koma wanzeru ali bwino+ kuposa mfumu yokalamba koma yopusa,+ imene sionanso kufunika kochenjezedwa.+