1 Samueli 17:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Nthawi yomweyo, Davide anasiya katundu+ wake m’manja mwa munthu wosamalira katundu,+ ndipo anathamangira kumalo omenyera nkhondo. Atafika kumeneko, anayamba kufunsa za abale ake ngati ali bwino.+
22 Nthawi yomweyo, Davide anasiya katundu+ wake m’manja mwa munthu wosamalira katundu,+ ndipo anathamangira kumalo omenyera nkhondo. Atafika kumeneko, anayamba kufunsa za abale ake ngati ali bwino.+