Salimo 37:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Usapse mtima ndipo pewa kukwiya.+Usapse mtima kuti ungachite choipa.+ Miyambo 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kuyankha modekha kumabweza mkwiyo,+ koma mawu opweteka amayambitsa mkwiyo.+ Mlaliki 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Usamafulumire kukwiya mumtima mwako,+ pakuti anthu opusa ndi amene sachedwa kupsa mtima.+